-
Chidziwitso
- 04,Mar 2024
- Posted By : icerim
- 0 Comments
Khonsolo ya mzindá wa zomba īkudziwitsa onse amene akupânga malonda a chimanga chachiwisi dowe/mondokwa) chootcha kapena сhophika kuti ndikosaloredwa kuchīta malondawa kuyambira lolemba pa 26th February, 2024.
Khonsoloyi yaletsa malondawa potsâtira malamūlo a maboma ang’onoangono (local government act, 1998). Ndiye dziwani kuti onse ochita malonda a chimanga chachiwisi munyengoyi adzaimbidwa mulandu.
Related