• Chidziwitso

    • 04,Mar 2024
    • Posted By : icerim
    • 0 Comments
    Khonsolo ya mzindá wa zomba īkudziwitsa onse amene akupânga malonda a chimanga chachiwisi dowe/mondokwa) chootcha kapena сhophika kuti ndikosaloredwa kuchīta malondawa kuyambira lolemba pa 26th February, 2024. Khonsoloyi yaletsa malondawa potsâtira malamūlo a maboma ang’onoangono (local government act, 1998). Ndiye dziwani kuti onse ochita malonda a chimanga chachiwisi munyengoyi adzaimbidwa mulandu.

Leave A Comment